17 Pamenepo Eli anayankha nati, Pita ndi mtendere; ndipo Mulungu wa Israyeli akupatse copempha cako unacipempha, kwa iye.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:17 nkhani