12 Ndipo munthu wina wa komweko anayankha nati, Ndipo atate wao ndiye yani? Cifukwa cace mauwa anakhala ngati mwambi, Kodi Saulinso ali mwa aneneri?
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10
Onani 1 Samueli 10:12 nkhani