14 Ndipo mbale wa atate wace wa Sauli ananena kwa iye ndi mnyamata wace, Munanka kuti? Ndipo iye anati, Kukafuna aburuwo; ndipo pakuona kuti sitinawapeza, tinadza kwa Samueli.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10
Onani 1 Samueli 10:14 nkhani