16 Ndipo Sauli anati kwa mbale wa atate wace, Anatiuza momveka kuti aburuwo anapezedwa kale. Koma sanamdziwitsa mau aja Samueli ananena zaufumuwo.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10
Onani 1 Samueli 10:16 nkhani