1 Samueli 10:19 BL92

19 koma lero inu mwakana Mulungu wanu amene anakupulumutsani yekha m'matsoka anu onse, ndi m'masautso anu; ndipo munanena naye, Koma mutipatse mfumu. Cifukwa cace tsono mudzionetse pamaso pa Mulungu mafuko mafuko, ndi magulu magulu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:19 nkhani