1 Samueli 10:23 BL92

23 Ndipo anathamanga, namtenga komweko; ndipo iye pamene anaima pakati pa anthuwo, anali wamtali koposa anthu onse anamlekeza m'cifuwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:23 nkhani