9 Ndipo kunali, pamene iye anapotoloka kuti alekane ndi Samueli, Mulungu anampatsa mtima wina watsopano; ndipo zizindikilo zija zonse zinacitika tsiku lija.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10
Onani 1 Samueli 10:9 nkhani