1 Samueli 12:23 BL92

23 Ndipo inenso, kukhale kutali ndi ine, kucimwira Yehova ndi kuleka kukupemphererani; koma ndidzakulangizani njira yabwino ndi yolungama.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:23 nkhani