1 Samueli 13:18 BL92

18 gulu lina linalowa njira yonka ku Betihoroni; ndi gulu linanso linalowa ku njira ya kumalire, akuyang'ana ku cigwa ca Zeboimu kucipululuko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:18 nkhani