1 Samueli 13:22 BL92

22 Comweco kunali kuti tsiku lankhondolo sunapezeka mkondo kapena lupanga m'manja a anthu onse anali ndi Sauli ndi Jonatani; koma Sauli yekha ndi Jonatani mwana wace anali nazo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:22 nkhani