1 Samueli 13:4 BL92

4 Ndipo Aisrayeli onse anamva kunena kuti Sauli anathyola kaboma ka Afilisti, ndi kuti Afilisti anyansidwa ndi Aisrayeli. Ndipo anthuwo anasonkhana kwa Sauli ku Giligala.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:4 nkhani