1 Samueli 14:10 BL92

10 Koma akatero kuti, Kwerani kuno kwa ife, tsono tidzakwera; pakuti Yehova wawapereka m'manja mwathu; ndipo ici cidzatikhalira cizindikilo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:10 nkhani