1 Samueli 14:17 BL92

17 Pamenepo Sauli ananena ndi anthu amene anali naye, Awerenge tsopano, kuti tizindikire anaticokera ndani. Ndipo pamene anawerenga, onani Jonatani ndi wonyamula zida zace panalibe.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:17 nkhani