1 Samueli 14:19 BL92

19 Ndipo kunali m'mene Sauli anali cilankhulire ndi wansembeyo, phokoso la m'cigono ca Afilisti linacitikabe, nilikula; ndipo Sauli ananena ndi wansembeyo, Bweza dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:19 nkhani