1 Samueli 14:24 BL92

24 Ndipo Aisrayeli anasauka tsiku lija; pakuti Sauli anawalumbirira, kuti, Atembereredwe iye wakudya kanthu kufikira madzulo, ndikabwezere cilango adani anga. Motero anthu onse anakhala opanda kudya.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:24 nkhani