1 Samueli 14:39 BL92

39 Pakuti, pali Yehova wakupulumutsa Israyeli, cingakhale ciri m'mwana wanga Jonatani, koma adzafa ndithu. Koma pakati pa anthu onse panalibe mmodzi wakumyankha iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:39 nkhani