1 Samueli 14:49 BL92

49 Ndipo ana a Sauli ndiwo Jonatani, ndi Isivi, ndi Malikisuwa; ndi maina a ana akazi ace awm ndi awa: dzina la woyamba ndiye Merabu, ndi dzina la mng'ono wace ndiye Mikala;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:49 nkhani