1 Samueli 14:7 BL92

7 Ndipo wonyamula zida zace ananena naye, Citani zonse ziri mumtima mwanu; palukani, onani ndiri pamodzi ndi inu monga mwa mtima wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:7 nkhani