1 Samueli 15:22 BL92

22 Ndipo Samueli anati, Kodi Yehova akondwera ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zophera, monga ndi kumvera mau a Yehova? Taonani, kumvera ndiko kokoma koposa nsembe, kuchera khutu koposa mafuta a nkhosa zamphongo,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:22 nkhani