1 Samueli 15:24 BL92

24 Ndipo Sauli anati kwa Samueli, Ndinacimwa; pakuti ndinalumpha lamulo la Yehova, ndi mau anu omwe; cifukwa ndinaopa anthuwo, ndi kumvera mau ao.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:24 nkhani