1 Samueli 15:28 BL92

28 Ndipo Samueli ananena naye, Yehova anang'amba ufumu wa Israyeli lero kuucotsa kwa inu, naupatsa kwa mnansi wanu wina wabwino woposa inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:28 nkhani