3 Muka tsopano, nukanthe Amaleki, nuononge konse konse zonse ali nazo, usawalekerere, koma uwaphe mwamuna ndi mkazi, mwana ndi woyamwa, ng'ombe ndi nkhosa, ngamila ndi buru.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15
Onani 1 Samueli 15:3 nkhani