1 Samueli 16:20 BL92

20 Ndipo Jese anatenga buru namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi: mwana wa mbuzi, nazitumiza kwa Sauli ndi Davide mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:20 nkhani