1 Samueli 16:7 BL92

7 Koma Yehova ananena ndi Samueli, Vsayang'ane nkhope yace, kapena kutalika kwa msinkhu wace, popeza Ine ndinamkana iye; pakuti Yehova saona monga aona munthu; pakuti munthu ayang'ana cooneka ndi maso, koma Yehova ayang'ana mumtima.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:7 nkhani