1 Samueli 17:13 BL92

13 Ndipo ana atatu akuru a Jese anatsata Sauli kunkhondoko; ndi maina ao a ana ace atatuwo adapita ku nkhondowo ndiwo Eliabu woyambayo, ndi mnzace womponda pamutu pace Abinadabu, ndi wacitatu Sama.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:13 nkhani