1 Samueli 17:23 BL92

23 Ndipo m'mene iye anali cilankhulire nao, onani cinakwerako ciwindaco, Mfilisti wa ku Gati, dzina lace ndiye Goliate, woturuka pakati pa mipambo ya Afilisti, nalankhula monga mau omwe aja; ndipo Davide anawamva.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:23 nkhani