1 Samueli 17:54 BL92

54 Ndipo Davide anatenga mutu wa Mfilistiyo, napita nao ku Yerusalemu; koma zida zace anazisunga m'hema wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:54 nkhani