57 Ndipo pamene Davide anabwera, atapha Mfilistiyo, Abineri anamtenga, nafika naye pamaso pa Sauli, mutu wa Mfilistiyo uli m'dzanja lace.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17
Onani 1 Samueli 17:57 nkhani