16 Koma Aisrayeli onse ndi Ayuda onse anamkonda Davide pakuti anawatsogolera kuturuka ndi kulowa nao.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18
Onani 1 Samueli 18:16 nkhani