1 Samueli 19:5 BL92

5 popeza iye anataya moyo wace nakantha Mfilistiyo, ndipo Yehova anacitira Aisrayeli onse cipulumutso cacikuru, inu munaciona, nimnnakondwera; tsono mudzacimwiranji mwazi wosalakwa, ndi kumupha Davide popanda cifukwa?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:5 nkhani