1 Ndipo Hana anapemphera, natiMtima wanga umyuka mokondwera kwa Yehova,Nyanga yanga yakwezeka mwa Yehova;Pakamwa panga pakula kwa adani anga;Popeza ndikondwera m'cipulumutsocanu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2
Onani 1 Samueli 2:1 nkhani