3 Musalankhulenso modzikuza kwambiri motero;M'kamwa mwanu musaturuke zolulutsa;Cifukwa Yehova ali Mulungu wanzeru,Ndipo iye ayesa zocita anthu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2
Onani 1 Samueli 2:3 nkhani