1 Samueli 20:1 BL92

1 Ndipo Davide anathawa ku Nayoti m'Rama, nadzanena pamaso pa Jonatani, Ndacitanji ine? kuipa kwanga kuli kotani? ndi chimo langa la pamaso pa atate wanu ndi ciani, kuti amafuna moyo wanga?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:1 nkhani