1 Samueli 20:17 BL92

17 Ndipo Jonatani anamlumbiritsa Davide kaciwiri, cifukwa anamkonda; popeza anamkonda monga anakonda moyo wa iye yekha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:17 nkhani