1 Samueli 20:3 BL92

3 Ndipo Davide analumbiranso nati, Atate wako adziwatu kuti wandikomera mtima; nati, Jonatani asadziwe ici, kuti angamve cisoni; koma pali Yehova, ndiponso pali moyo wako, pakati pa ine ndi imfa pali ngati phazilimodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:3 nkhani