1 Samueli 20:36 BL92

36 Ndipo anauza mnyamata waceyo, Thamanga uzikatola mibvi Imene ndidzaponya; ndipo analikuthamanga mnyamatayu, iye anaponya mubvi kuutumphitsa iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:36 nkhani