1 Samueli 20:38 BL92

38 Ndipo Jonatani anapfuulira mnyamatayo, nati, Yendesa, fulumira, usaima. Ndi mnyamata wa Jonatani anatola mibvi, nafika kwa mbuye wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:38 nkhani