1 Samueli 21:13 BL92

13 Nasanduliza makhalidwe ace pamaso pao, nadzionetsera m'manja mwao ngati wamisala, nangolembalemba pa zitseko za cipata, nakhetsa dobvu lace pa ndebvu yace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:13 nkhani