1 Samueli 21:4 BL92

4 Ndipo wansembeyo anayankha Davide nati, Ndiribe mkate wacabe, koma ulipo mkate wopatulika; pokhapo ngati anyamatawo anadzisunga kupewa akazi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:4 nkhani