1 Samueli 22:17 BL92

17 Mfumu niuza asilikari akuima comzinga iye, Potolokani, iphani ansembe a Yehova; cifukwa agwirizana ndi Davide, ndipo anadziwa kuti alinkuthawa, koma sanandiululira. Koma anayamata a mfumu sanafuna kutambalitsa manja ao kupha ansembe a Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:17 nkhani