1 Samueli 22:2 BL92

2 Ndipo yense wosautsidwa, ndi yense wa ngongole, ndi yense wowawidwa mtima, anaunjikana kwa iye; iye nakhala mtsogoleri wao; ndipo anali nao anthu ngati mazana anai.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:2 nkhani