1 Samueli 23:10 BL92

10 Nati Davide, Yehova, Mulungu wa Israyeli, mnyamata wanu wamva zoona kuti Sauli afuna kudza ku Keila, kuononga mudziwo cifukwa ca ine.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:10 nkhani