1 Samueli 23:12 BL92

12 Tsono Davide anati, Kodi amuna a ku Keila adzandipereka ine ndi anyamata anga m'dzanja la Sauli? Ndipo Yehova anati, Adzakupereka.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:12 nkhani