1 Samueli 23:28 BL92

28 Comweco Sauli anabwerera polondola Davide, nakakomana ndi Afilisti; cifukwa cace anachula dzina lace la malo aja, Thanthwe lolekanitsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:28 nkhani