1 Samueli 24:10 BL92

10 Onani, lero lomwe maso anu anapenya kuti Yehova anakuperekani inu lero m'dzanja langa m'phangamo, ndipo ena anandiuza ndikupheni; koma ndinakulekani, ndi kuti, Sindidzatukulira mbuye wanga dzanja langa; cifukwa iye ndiye wodzozedwa wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:10 nkhani