1 Samueli 24:12 BL92

12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu; ndipo Yehova adzandibwezera cilango kwa inu; koma dzanja langa silidzakhala pa inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:12 nkhani