19 Pakuti munthu akapeza mdani wace, adzamleka kodi kuti acoke bwino? Cifukwa cace Yehova akubwezere zabwino pa ici unandicitira ine lero lomwe.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24
Onani 1 Samueli 24:19 nkhani