1 Samueli 24:21 BL92

21 Cifukwa cace tsono undilumbirire ndi Yehova, kuti sudzatha mbeu yanga nditamuka ine, ndi kuti sudzaononga dzina langa m'nyumba ya atate wanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:21 nkhani