1 Samueli 24:3 BL92

3 Ndipo panjira anafika ku makola a nkhosa, kumene kunali phanga; ndipo Sauli analowa kuti akapfunde mapazi ace. Ndipo Davide ndi anyamata ace analikukhala m'kati mwa phangamo,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:3 nkhani