1 Samueli 25:15 BL92

15 Koma anthu aja anaticitira zabwino ndithu, sanaticititsa manyazi, ndi panalibe kanthu kadatisowa, nthawi zonse tinali kuyenderana nao kubusa kuja;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:15 nkhani